Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 17:5 - Buku Lopatulika

5 Iye wakupereka mabwenzi ake ku ukapolo, m'maso mwa ana ake mudzada.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Iye wakupereka mabwenzi ake ku ukapolo, m'maso mwa ana ake mudzada.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Paja akuti munthu akapereka abwenzi ake chifukwa cha chuma, ana ake amazunzika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ngati munthu apereka mnzake chifukwa cha chuma, ana ake sadzaona mwayi.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 17:5
12 Mawu Ofanana  

Koma m'masiku ako sindidzatero chifukwa cha Davide atate wako, koma ndidzaung'ambira m'manja mwa mwana wako;


Koma maso a oipa adzagoma, ndi pothawirapo padzawasowa, ndipo chiyembekezo chao ndicho kupereka mzimu wao.


Usazipembedzere izo, usazitumikire izo; chifukwa Ine Yehova Mulungu wako ndili Mulungu wansanje, wakulanga ana chifukwa cha atate ao, kufikira mbadwo wachitatu ndi wachinai wa iwo amene akudana ndi Ine;


Kazitape woyendayenda awanditsa zinsinsi; usadudukire woyasama milomo yake.


Wosyasyalika mnzake atcherera mapazi ake ukonde.


Maso athu athedwa, tikali ndi moyo, poyembekeza thandizo chabe; kudikira tinadikira mtundu wosatha kupulumutsa.


Usamasautsa mnansi wako, kapena kulanda zake; mphotho yake ya wolipidwa isakhale ndi iwe kufikira m'mawa.


Usamayendayenda nusinjirira mwa anthu a mtundu wako; usamatsata mwazi wa mnansi wako; Ine ndine Yehova.


Ndipo mwa a mitundu iyi simudzapumula, inde sipadzakhala popumulira phazi lanu; koma Yehova adzakupatsani kumeneko mtima wonjenjemera, m'maso mwanu mudzada, mudzafa ndi kulefuka mtima.


Pakuti sitinayende nao mau osyasyalika nthawi iliyonse monga mudziwa, kapena kupsinjika msiriro, mboni ndi Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa