Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 17:3 - Buku Lopatulika

3 Mupatse chigwiriro tsono, mundikhalire chikole Inu nokha kwanu; ndani adzapangana nane kundilipirira?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mupatse chigwiriro tsono, mundikhalire chikole Inu nokha kwanu; ndani adzapangana nane kundilipirira?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 “Inu nokha Mulungu, mukhale ngati chigwiriro changa. Kulibenso wina woti nkunditchinjiriza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 “Inu Mulungu, patseni chikole chimene mukufuna. Ndani wina amene adzandiperekera ine chikole?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 17:3
12 Mawu Ofanana  

Ine ndidzakhala chikole, pa manja anga mudzamfunsa: ndikapanda kumbwezera kwa inu ndi kumuimitsa pamaso panu, chifukwa chake chidzakhala pa ine masiku onse:


Pakuti kapolo wanu anadziyesa chikole cha mnyamata pa atate wanga, kuti, Ndikapanda kumbwezeranso kwa inu, pamenepo ndidzakhala ndi chifukwa kwa atate wanga nthawi zonse.


Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo?


Palibe wakutiweruza, wakutisanjika ife tonse awiri manja ake.


Mumkhalire chikole mtumiki wanu chimkomere; odzikuza asandisautse.


Woperekera mlendo chikole adzaphwetekwapo; koma wakuda chikole akhala ndi mtendere.


Munthu wosowa nzeru apangana kulipirira wina, napereka chikole pamaso pa mnzake.


Tenga malaya a woperekera mlendo chikole; woperekera mkazi wachilendo chikole umgwire mwini.


Usakhale wodulirana mpherere, ngakhale kumperekera chikole cha ngongole zake.


ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala, ndi kusauka kwako ngati munthu wachikopa.


Ndinalankhulalankhula ngati namzeze, pena chumba; Ndinalira maliro ngati nkhunda; maso anga analephera pogadamira kumwamba. Ambuye ndasautsidwa, mundiperekere chikoli.


Momwemonso Yesu wakhala Nkhoswe ya pangano loposa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa