Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 16:7 - Buku Lopatulika

7 Koma tsopano wandilemetsa Iye; mwapasula msonkhano wanga wonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Koma tsopano wandilemetsa Iye; mwapasula msonkhano wanga wonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ndithudi, Mulungu wanditha mphamvu, waononga banja langa lonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndithudi, Inu Mulungu mwanditha mphamvu; mwawononga banja langa lonse.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 16:7
13 Mawu Ofanana  

Mtima wanga ulema nao moyo wanga, ndidzadzilolera kudandaula kwanga, ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga.


Mabwenzi anga andinyoza; koma diso langa lilirira misozi kwa Mulungu.


Iye anandichotsera abale anga kutali, ndi odziwana nane andiyesa mlendo konse.


Apo oipa aleka kumavuta; ndi apo ofooka mphamvu akhala m'kupumula.


Mulibe thandizo mwa ine ndekha; chipulumutso chandithawa.


Ndinyansidwa nao moyo wanga; sindidzakhala ndi moyo chikhalire; mundileke; pakuti masiku anga ndi achabe.


momwemo anandilowetsa miyezi yopanda pake. Nandiikiratu zowawa usiku ndi usiku.


Ambuye Yehova wandipatsa Ine lilime la ophunzira, kuti ndidziwe kunena mau akuchirikiza iye amene ali wolema. Iye andigalamutsa m'mawa ndi m'mawa, nagalamutsa khutu langa kuti limve monga ophunzira.


Chifukwa chake Inenso ndakukantha ndi kukupweteketsa; ndakupulula chifukwa cha zochimwa zako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa