Yobu 16:6 - Buku Lopatulika6 Chinkana ndinena chisoni changa sichitsika; ndipo ndikaleka, chindichokera nchiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chinkana ndinena chisoni changa sichitsika; ndipo ndikaleka, chindichokera nchiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 “Ine ndikati ndilankhule, zoŵaŵa zanga sizichepa. Ndikati ndikhale chete, zoŵaŵazo zikhala zilipobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Koma ine ndikati ndiyankhule ululu wanga sukuchepa; ndipo ndikati ndikhale chete, ululu wanga sukuchokabe. Onani mutuwo |