Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 16:3 - Buku Lopatulika

3 Kodi adzatha mau ouluzika? Kapena chikuwindula nchiyani kuti uyankha zotere?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Kodi adzatha mau ouluzika? Kapena chikuwindula nchiyani kuti uyankha zotere?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kodi mudzakhala mukulankhulabe mau achabechabeŵa mpaka liti? Kaya chakuvutani nchiyani kuti muzilankhulabe mau otsutsaŵa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi mawu anu ochulukawo adzatha? Kodi chikukuvutani nʼchiyani kuti muzingoyankhula mawu otsutsawa?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 16:3
10 Mawu Ofanana  

Kodi mwini nzeru ayankhe ndi kudziwa kouluzika, ndi kudzaza mimba yake ndi mphepo ya kum'mawa?


Ndamva kudzudzula kwakundichititsa manyazi, ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.


Taonani, inu nonse munachiona; ndipo mugwidwa nazo zopanda pake chifukwa ninji?


Kodi muyesa kudzudzula mau? Popeza maneno a munthu wodololoka akunga mphepo.


Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?


Ndipo sanalimbike mtima munthu aliyense kumfunsa kanthu kuyambira tsiku lomwelo.


amene ayenera kutsekedwa pakamwa; ndiwo amene apasula mabanja banja lonse, ndi kuphunzitsa zosayenera chifukwa cha chisiriro chonyansa.


mau olama osatsutsika; kuti iye wakutsutsana achite manyazi, posakhala nako kanthu koipa kakutinenera ife.


Ndipo popeza munthuyo adatero chaka ndi chaka, popita mkaziyo kunyumba ya Yehova, mnzakeyo amamputa; chifukwa chake iye analira misozi, nakana kudya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa