Yobu 15:9 - Buku Lopatulika9 Udziwa chiyani, osachidziwa ife? Uzindikira chiyani, chosakhala mwa ife? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Udziwa chiyani, osachidziwa ife? Uzindikira chiyani, chosakhala mwa ife? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kodi nchiyani chimene umadziŵa iwe, chosachidziŵa ife? Kodi chilipo chimene umamvetsa iwe, chosachimvetsa ife? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kodi iwe umadziwa chiyani chimene ife sitichidziwa? Kodi iwe uli ndi chidziwitso chanji chimene ife tilibe? Onani mutuwo |