Yobu 13:8 - Buku Lopatulika8 Kodi mukhalira kumodzi ndi Iye? Kodi mungamuimilire Mulungu pa mlandu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Kodi mukhalira kumodzi ndi Iye? Mundilimbirana mwa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kodi mukuti mukondere Mulungu? Kodi mukuti muteteze Mulungu pa mlandu wake? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kodi mudzaonetsa kuti Iyeyo ngokondera? Kodi inu mudzamuteteza Mulungu pa mlandu wake? Onani mutuwo |