Yobu 13:6 - Buku Lopatulika6 Tamvani tsono kudzikanira kwanga, tamverani kudzinenera kwa milomo yanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Tamvani tsono kudzikanira kwanga, tamverani kudzinenera kwa milomo yanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono mumve zimene nditi ndinene, mumvere mau anga ofotokoza za mlandu wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Tsopano imvani kudzikanira kwanga; imvani kudandaula kwa pakamwa panga. Onani mutuwo |