Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 13:5 - Buku Lopatulika

5 Mwenzi mutakhala chete konse, ndiko kukadakhala nzeru zanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mwenzi mutakhala chete konse, ndiko kukadakhala nzeru zanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Achikhala munangokhala chete, apo mukadachita zanzeru

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Achikhala munangokhala chete nonsenu! Apo mukanachita zanzeru.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 13:5
14 Mawu Ofanana  

Kodi zotamanda zako ziwatseke anthu pakamwa? Useka kodi, wopanda munthu wakukuchititsapo manyazi?


Khalani chete, ndilekeni, kuti ndinene, chondifikira chifike.


Tamvani tsono kudzikanira kwanga, tamverani kudzinenera kwa milomo yanga.


Kodi adzatha mau ouluzika? Kapena chikuwindula nchiyani kuti uyankha zotere?


Musaka mau kufikira liti? Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena.


Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti, ndi kundithyolathyola nao mau?


Ndiyang'anireni, nimusumwe, gwirani pakamwa panu.


Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pake pa iye mwini.


Kodi ndidzangolindira popeza sanena iwo, popeza akhala duu osayankhanso?


Ngakhale chitsiru chikatonthola achiyesa chanzeru; posunama ali wochenjera.


Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno.


Chifukwa chake wochenjerayo akhala chete nthawi yomweyo; pakuti ndiyo nthawi yoipa.


Mudziwa, abale anga okondedwa, kuti munthu aliyense akhale wotchera khutu, wodekha polankhula, wodekha pakupsa mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa