Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 13:3 - Buku Lopatulika

3 Koma ine ndidzanena ndi Wamphamvuyonse, ndipo ndifuna kudzikanira kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Koma ine ndidzanena ndi Wamphamvuyonse, ndipo ndifuna kudzikanira kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Koma ine ndikadakonda kulankhula ndi Mphambe, ndikadakonda kukamba naye Mulungu za mlandu wanga pamasompamaso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Koma ine ndikulakalaka nditayankhula ndi Wamphamvuzonse ndi kukamba mlandu wanga ndi Mulungu.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 13:3
14 Mawu Ofanana  

Koma, ha? Mwenzi atanena Mulungu, ndi kukutsegulira milomo yake motsutsa;


Angakhale andipha koma ndidzamlindira; komanso ndidzaumirira mayendedwe anga pamaso pake.


Pamenepo muitane, ndipo ndidzayankha; kapena ndinene ndine, ndipo mundiyankhe ndinu.


Ha! Ndikadakhala naye wina wakundimvera, chizindikiro changa sichi, Wamphamvuyonse andiyankhe; mwenzi ntakhala nao mau akundineneza analemberawo mdani wanga!


Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wochita makani ndi Mulungu ayankhe.


Koma ine ndikadafuna Mulungu, ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;


Akafuna Iye kutsutsana naye, sadzambwezera Iye mau amodzi onse mwa chikwi.


Onetsani mlandu wanu, ati Yehova; tulutsani zifukwa zanu zolimba, ati mfumu ya Yakobo.


Tamverani, mapiri inu, chitsutsano cha Yehova, ndi inu maziko olimba a dziko lapansi; pakuti Yehova ali nacho chitsutsano ndi anthu ake, ndipo adzatsutsana ndi Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa