Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 13:2 - Buku Lopatulika

2 Chimene muchidziwa inu, inenso ndichidziwa; sindikucheperani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Chimene muchidziwa inu, inenso ndichidziwa; sindikucheperani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Zimene inu mumadziŵa, inenso ndimazidziŵa. Inu simundipambana ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Zimene inu mukudziwa, inenso ndimazidziwa; ineyo sindine munthu wamba kwa inu.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 13:2
12 Mawu Ofanana  

Koma inenso ndili nayo nzeru monga inu. Sindingakuchepereni; ndani sadziwa zonga izi?


Yobu alankhula wopanda kudziwa, ndi mau ake alibe nzeru.


chifukwa chake Yobu anatsegula pakamwa pake mwachabe, nachulukitsa mau opanda nzeru.


Mvetsetsani chibumo cha mau ake, ndi kugunda kotuluka m'kamwa mwake.


Kunali tsono atanena Yehova mau awa kwa Yobu, Yehova anati kwa Elifazi wa ku Temani, Mkwiyo wanga wakuyakira iwe ndi mabwenzi ako awiri, pakuti simunandinenere choyenera monga ananena mtumiki wanga Yobu.


Koma ine ndikadafuna Mulungu, ndikadaikira mlandu wanga Mulungu;


Ndakhala wopanda nzeru, mwandichititsa kutero; pakuti inu munayenera kundivomereza; pakuti sindiperewere ndi atumwi oposatu m'kanthu konse, ndingakhale ndili chabe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa