Yobu 12:3 - Buku Lopatulika3 Koma inenso ndili nayo nzeru monga inu. Sindingakuchepereni; ndani sadziwa zonga izi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma inenso ndili nayo nzeru monga inu. Sindingakuchepereni; ndani sadziwa zonga izi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma inenso ndili nazo nzeru ngati inu nomwe. Inu simundipambana, ai. Aliyense amadziŵa zonse mwanenazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma inenso ndili nazo nzeru ngati inu; ineyo sindine munthu wamba kwa inu. Ndani amene sadziwa zonse zimene mwanenazi? Onani mutuwo |