Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 11:5 - Buku Lopatulika

5 Koma, ha? Mwenzi atanena Mulungu, ndi kukutsegulira milomo yake motsutsa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma, ha? Mwenzi atanena Mulungu, ndi kukutsegulira milomo yake motsutsa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Koma ha, achikhala Mulungu adaalankhula, achikhala adaakudzudzula,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Aa, nʼkanakonda Mulungu akanayankhula kuti Iye atsekule pakamwa pake kutsutsana nawe

Onani mutuwo Koperani




Yobu 11:5
9 Mawu Ofanana  

Pakuti unena, Chiphunzitso changa nchoona, ndipo ndili woyera pamaso pako.


nakufotokozere zinsinsi za nzeru, popeza zipindikapindika machitidwe ao! Chifukwa chake dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.


Ha! Ndikadakhala naye wina wakundimvera, chizindikiro changa sichi, Wamphamvuyonse andiyankhe; mwenzi ntakhala nao mau akundineneza analemberawo mdani wanga!


Chingakhale chiweruzo changa udzachithyola kodi? Udzanditsutsa kuti ndili woipa kodi, kuti ukhale wolungama ndiwe?


Kunali tsono atanena Yehova mau awa kwa Yobu, Yehova anati kwa Elifazi wa ku Temani, Mkwiyo wanga wakuyakira iwe ndi mabwenzi ako awiri, pakuti simunandinenere choyenera monga ananena mtumiki wanga Yobu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa