Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 11:2 - Buku Lopatulika

2 Kodi mau ochulukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Kodi mau ochulukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Kodi mau ambirimbiriŵa nkukhala osaŵayankha? Kodi kulongolola nkumulungamitsa munthu?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Kodi mawu ambirimbiriwa nʼkukhala osayankhidwa? Kodi munthu woyankhulayankhulayu nʼkulungamitsidwa?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 11:2
11 Mawu Ofanana  

Pamenepo anayankha Zofari wa ku Naama, nati,


Kodi mwini nzeru ayankhe ndi kudziwa kouluzika, ndi kudzaza mimba yake ndi mphepo ya kum'mawa?


Kodi adzatha mau ouluzika? Kapena chikuwindula nchiyani kuti uyankha zotere?


Musaka mau kufikira liti? Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena.


Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?


Munthu wamlomo sadzakhazikika padziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse.


Pochuluka mau zolakwa sizisoweka; koma wokhala chete achita mwanzeru.


Samalira phazi lako popita kunyumba ya Mulungu; pakuti kuyandikira kumvera kupambana kupereka nsembe za zitsiru; pakuti sizizindikira kuti zilikuchimwa.


Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno.


Ndipo akukonda nzeru ena a Epikurea ndi a Stoiki anatengana naye. Ena anati, Ichi chiyani afuna kunena wobwetuka uyu? Ndipo ena, Anga wolalikira ziwanda zachilendo, chifukwa analalikira Yesu ndi kuuka kwa akufa.


Mudziwa, abale anga okondedwa, kuti munthu aliyense akhale wotchera khutu, wodekha polankhula, wodekha pakupsa mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa