Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 10:8 - Buku Lopatulika

8 Manja anu anandiumba, nandiulunga monsemu, koma mufuna kundiononga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Manja anu anandiumba, nandiulunga monsemu, koma mufuna kundiononga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 “Mudandiwumba ndi kundipanga ndi manja anu. Koma tsopano mukufuna kundiwononga ndi manja anu omwewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 “Munandiwumba ndi kundipanga ndi manja anu. Kodi tsopano Inu mudzatembenuka ndi kundiwononga?

Onani mutuwo Koperani




Yobu 10:8
14 Mawu Ofanana  

Chikukomerani kodi kungosautsa, kuti mupeputsa ntchito yolemetsa manja anu, ndi kuti muwalira pa uphungu wa oipa?


Ndaniyo adzatsutsana nane? Ndikakhala chete, ndidzapereka mzimu wanga.


Pakuti ndidziwa kuti mudzandifikitsa kuimfa, ndi kunyumba yokomanamo amoyo onse.


Pakuti andithyola ndi mkuntho, nachulukitsa mabala anga kopanda chifukwa.


Kuli chimodzimodzi monsemo, m'mwemo ndikuti Iye aononga wangwiro ndi woipa pamodzi.


Dziwani kuti Yehova ndiye Mulungu; Iyeyu anatilenga, ndipo ife ndife ake; ndife anthu ake ndi nkhosa zapabusa pake.


Manja anu anandilenga nandiumba; mundizindikiritse, kuti ndiphunzire malemba anu.


Yehova adzanditsirizira za kwa ine: Chifundo chanu, Yehova, chifikira kunthawi zonse: Musasiye ntchito za manja anu.


Thupi langa silinabisikire Inu popangidwa ine mobisika, poombedwa ine monga m'munsi mwake mwa dziko lapansi.


Ndisanaumbidwe ine maso anu anandipenya, ziwalo zanga zonse zinalembedwa m'buku mwanu, masiku akuti ziumbidwe, pakalibe chimodzi cha izo.


Iye amene akonza mitima ya iwo onse, amene azindikira zochita zao zonse.


yense wotchedwa dzina langa, amene ndinamlenga chifukwa cha ulemerero wanga; ndinamuumba iye; inde, ndinampanga iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa