Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 10:2 - Buku Lopatulika

2 Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; mundidziwitse chifukwa cha kutsutsana nane.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; mundidziwitse chifukwa cha kutsutsana nane.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ndidzauza Mulungu kuti, Inu Mulungu, musandiweruze kuti ndine wolakwa. Koma mundidziŵitse chifukwa chimene mukukanganirana nane.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndidzati kwa Mulungu wanga: Musandiweruze kuti ndine wolakwa, koma mundiwuze chifukwa chimene Inu mukukanganira ndi ine.

Onani mutuwo Koperani




Yobu 10:2
20 Mawu Ofanana  

Mphulupulu zanga ndi zochimwa zanga ndi zingati? Mundidziwitse kulakwa kwanga ndi tchimo langa.


Kodi ine, kudandaula kwanga, ndidandaulira munthu? Ndipo ndilekerenji kupsa mtima?


Mutsutsana ndi Iye chifukwa ninji? Popeza pa zake zonse sawulula chifukwa.


Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wochita makani ndi Mulungu ayankhe.


Ngati ndachimwa, ndingachitire Inu chiyani, Inu wodikira anthu? Mwandiikiranji ndikhale chandamali chanu? Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?


Mlandu udzanditsutsa; potero ndigwire ntchito chabe chifukwa ninji?


Akafuna Iye kutsutsana naye, sadzambwezera Iye mau amodzi onse mwa chikwi.


Koma Inu, Yehova Ambuye, muchite nane chifukwa cha dzina lanu; ndilanditseni popeza chifundo chanu ndi chabwino.


Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu; pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense.


Musakumbukire zolakwa za ubwana wanga kapena zopikisana nanu. Mundikumbukire monga mwa chifundo chanu, chifukwa cha ubwino wanu, Yehova.


Imvani, Yehova, liu langa pofuula ine; mundichitirenso chifundo ndipo mundivomereze.


Chifukwa chake tsopano iwo akukhala mwa Khristu Yesu alibe kutsutsidwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa