Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yobu 1:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo anabala ana aamuna asanu ndi awiri, ndi ana aakazi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo anabala ana amuna asanu ndi awiri, ndi ana akazi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Anali ndi ana aamuna asanu ndi aŵiri, ndi ana aakazi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Anali ndi ana aamuna asanu ndi awiri ndi ana aakazi atatu,

Onani mutuwo Koperani




Yobu 1:2
8 Mawu Ofanana  

Nawawerengera Hamani kulemera kwake kwakukulu, ndi ana ake ochuluka, ndi zonse mfumu idamkuza nazo, ndi umo adamkweza koposa akalonga ndi anyamata a mfumu.


Khalani chete, ndilekeni, kuti ndinene, chondifikira chifike.


Ndipo Yehova anachotsa ukapolo wa Yobu, pamene anapempherera mabwenzi ake; Yehova nachulukitsa zake zonse za Yobu mpaka kuziwirikiza.


Ndipo Yehova anadalitsa chitsiriziro cha Yobu koposa chiyambi chake, ndipo anali nazo nkhosa zikwi khumi ndi zinai, ndi ngamira zikwi zisanu ndi chimodzi, ndi ng'ombe zamagoli chikwi chimodzi, ndi abulu aakazi chikwi chimodzi.


Anali naonso ana aamuna asanu ndi awiri ndi ana aakazi atatu.


Ndipo awadalitsa, kotero kuti achuluka kwambiri; osachepsanso zoweta zao.


Mkazi wako adzanga mpesa wopatsa m'mbali za nyumba yako; ana ako adzanga timitengo ta azitona pozinga podyera pako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa