Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yesaya 8:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo ndidzadzitengera ine mboni zokhulupirika, Uriya wansembe, ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo ndidzadzitengera ine mboni zokhulupirika, Uriya wansembe, ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Tsono ndidapeza mboni zokhulupirika, wansembe Uriya ndiponso Zekariya mwana wa Yeberekiya, kuti andichitire umboni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndipo ndidzayitana wansembe Uriya ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya kuti akhale mboni zanga zodalirika.”

Onani mutuwo Koperani




Yesaya 8:2
8 Mawu Ofanana  

Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai mu Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Abi mwana wa Zekariya.


Manga umboni, mata chizindikiro pachilamulo mwa ophunzira anga.


Ndipo ndinalemba chikalatacho, ndichisindikiza, ndiitana mboni zambiri, ndiyesa ndalama m'miyeso.


Nthawi yachitatu iyi ndilinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika.


Ndipo anatenga amuna khumi a akulu a mzinda, nati, Mukhale pansi apa. Nakhala pansi iwo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa