Yesaya 3:3 - Buku Lopatulika3 kapitao wa makumi asanu, ndi munthu wolemekezeka, ndi phungu, ndi mmisiri waluso, ndi wodziwa matsenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 kapitao wa makumi asanu, ndi munthu wolemekezeka, ndi mphungu, ndi mmisiri waluso, ndi wodziwa matsenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 atsogoleri ankhondo ndi anthu olemekezeka, aphungu ndi amatsenga, ndiponso akatswiri a njirisi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 atsogoleri a ankhondo makumi asanu ndi anthu olemekezeka, aphungu ndi anthu amatsenga ndi akatswiri pa za kulosera. Onani mutuwo |