Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yesaya 3:2 - Buku Lopatulika

2 munthu wamphamvu, ndi munthu wankhondo; woweruza ndi mneneri, ndi waula, ndi nkhalamba;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 munthu wamphamvu, ndi munthu wankhondo; woweruza ndi mneneri, ndi waula, ndi nkhalamba;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 anthu amphamvu ndi asilikali ankhondo, aweruzi ndi aneneri, olosa ndi akuluakulu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 anthu amphamvu ndi asilikali ankhondo, oweruza ndi aneneri, anthu olosera ndi akuluakulu,

Onani mutuwo Koperani




Yesaya 3:2
12 Mawu Ofanana  

Ndipo Aisraele onse anawerengedwa mwa chibadwidwe chao; ndipo taonani, alembedwa m'buku la mafumu a Israele; ndipo Yuda anatengedwa ndende kunka ku Babiloni chifukwa cha kulakwa kwao.


Sitiziona zizindikiro zathu; palibenso mneneri; ndipo mwa ife palibe wina wakudziwa mpaka liti.


kapitao wa makumi asanu, ndi munthu wolemekezeka, ndi phungu, ndi mmisiri waluso, ndi wodziwa matsenga.


Uziti, tsono kwa nyumba ya mpandukoyi, Simudziwa kodi izi nchiyani? Uziti, Taonani mfumu ya ku Babiloni inadza ku Yerusalemu, nkutenga mfumu yake ndi akalonga ake, nkubwera nao kuli iye ku Babiloni;


ndipo inatenga wa mbumba yachifumu, nkuchita naye pangano, nkumlumbiritsa, nkuchotsa amphamvu a m'dziko;


Pamenepo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, wapenya kodi chochita akulu a nyumba ya Israele mumdima, aliyense m'chipinda chake cha zifanizo? Pakuti ati, Yehova satipenya, Yehova wataya dziko.


Nati kwa enawo, ndilikumva ine, Pitani pakati pa mzinda kumtsata iye, ndi kukantha; maso anu asalekerere, musachite chifundo;


ndipo ndidzalikha woweruza pakati pake, ndi kupha akalonga ake onse, ati Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa