Yeremiya 9:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Yehova ati, Chifukwa asiya chilamulo changa ndinachiika pamaso pao, ndipo sanamvere mau anga, osayenda m'menemo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Yehova ati, Chifukwa asiya chilamulo changa ndinachiika pamaso pao, ndipo sanamvera mau anga, osayenda m'menemo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Apo Chauta adayankha kuti, “Nchifukwa chakuti anthu angawo sadatsate malamulo amene ndidaŵapatsa, ndipo sadamvere mau anga ndi kuŵasamala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yehova anati, “Nʼchifukwa chakuti anthuwa analeka kutsata malamulo anga amene ndinawapatsa; sanandimvere kapena kuwasamala. Onani mutuwo |