Yeremiya 8:17 - Buku Lopatulika17 Pakuti, taonani, ndidzatumiza pa inu njoka, mphiri, zosalola kuitanidwa; ndipo zidzakulumani inu, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pakuti, taonani, ndidzatumiza pa inu njoka, mphiri, zosalola kuitanidwa; ndipo zidzakulumani inu, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Onani, ndikukutumirani njoka, mphiri zimene munthu sangazilodze, ndipo zidzakulumani,” akuterotu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Yehova akuti, “Onani, ndikukutumizirani njoka zaululu, mphiri zimene munthu sangathe kuzilodza, ndipo zidzakulumani,” Onani mutuwo |