Yeremiya 7:22 - Buku Lopatulika22 Pakuti sindinanena kwa makolo anu, tsiku lija ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, ngakhale kuwauza nsembe zopsereza kapena zophera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Pakuti sindinanena kwa makolo anu, tsiku lija ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, ngakhale kuwauza nsembe zopsereza kapena zophera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pamene ndidatulutsa makolo anu ku dziko la Ejipito, sindidaŵalamule kuti azipereka nsembe zopsereza kapena nsembe zina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pakuti pamene ndinatulutsa makolo anu ku Igupto ndi kuyankhula nawo, sindinawalamulire kuti azipereka nsembe zopsereza kapena nsembe zinazo, Onani mutuwo |