Yeremiya 7:21 - Buku Lopatulika21 Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele; Ikani zopereka zopsereza zanu pa nsembe zophera zanu, nimudye nyama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele; Ikani zopereka zopsereza zanu pa nsembe zophera zanu, nimudye nyama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, akunena kuti, “Muwonjeze zopereka zanu zopsereza pa nsembe zanu zinazo, ndipo mudye nyama yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 “Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti: Wonjezerani nsembe zanu zopsereza pa nsembe zanu zinazo ndipo mudye nyama yakeyo! Onani mutuwo |