Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 6:18 - Buku Lopatulika

18 Chifukwa chake tamverani, amitundu inu, dziwani, msonkhano inu, chimene chili mwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Chifukwa chake tamverani, amitundu inu, dziwani, msonkhano inu, chimene chili mwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Nchifukwa chake imvani inu anthu a mitundu ina, penyetsetsani, inu mwasonkhana panonu, zimene zidzaŵagwere anthuwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Nʼchifukwa chake imvani, inu anthu a mitundu ina; yangʼanitsitsani, inu amene mwasonkhana pano, chimene chidzawachitikire anthuwo.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 6:18
9 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, inu okhala mu Yerusalemu, ndi anthu a Yuda, weruzanitu mlandu wa ine ndi munda wanga wampesa.


Tamvani mau a Yehova, amitundu inu, lalikirani m'zisumbu zakutali; ndi kuti, Iye amene anabalalitsa Israele adzasonkhanitsa, nadzamsunga, monga mbusa achita ndi zoweta zake.


Ndipo ndinati, Ha, Yehova Mulungu! Ndithu mwanyenga kwambiri anthu awa ndi Yerusalemu, ndi kuti, Mudzalandira mtendere; koma lupanga lafikira pamoyo.


Mukumbutse mitundu ya anthu; taonani, lalikirani Yerusalemu, kuti owazinga ndi nkhondo afumira kudziko lakutali, nainenera mizinda ya Yuda mau ao.


Ndipo ndinaika alonda oyang'anira inu, ndi kuti, Mverani mau a lipenga; koma anati, Sitidzamvera.


Tamva, dziko lapansi iwe; taona, Ine ndidzatengera choipa pa anthu awa, chipatso cha maganizo ao, pakuti sanamvere mau anga, kapena chilamulo changa, koma wachikana.


Anthu anga, kumbukiranitu chofunsira Balaki mfumu ya Mowabu, ndi chomuyankha Balamu mwana wa Beori, kuyambira ku Sitimu kufikira ku Giligala; kuti mudziwe zolungama za Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa