Yeremiya 52:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo mzinda unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo mudzi unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Motero mzindawo udaazingidwa ndi zithandozo mpaka chaka cha 11 cha ufumu wa Zedekiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mzindawo unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha ulamuliro wa Mfumu Zedekiya. Onani mutuwo |