Yeremiya 52:34 - Buku Lopatulika34 Koma phoso lake mfumu ya ku Babiloni sanaleke kumpatsa, phoso tsiku ndi tsiku gawo lake, mpaka tsiku la kufa kwake, masiku onse a moyo wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma phoso lake mfumu ya ku Babiloni sanaleke kumpatsa, phoso tsiku ndi tsiku gawo lake, mpaka tsiku la kufa kwake, masiku onse a moyo wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Kunena za phoso, mfumu ya ku Babiloni inkampatsa Yehoyakimu phoso lake tsiku ndi tsiku mpaka kufa kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Tsiku ndi tsiku mfumu ya ku Babuloni inkamupatsa Yehoyakini phoso lake nthawi yonse ya moyo wake, mpaka pa nthawi ya imfa yake. Onani mutuwo |