Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 52:32 - Buku Lopatulika

32 nanena naye bwino, naika mpando wake upose mipando ya mafumu amene anali naye mu Babiloni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 nanena naye bwino, naika mpando wake upose mipando ya mafumu amene anali naye m'Babiloni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Adalankhula naye mwachifundo, nampatsa malo aulemu kuposa mafumu ena amene anali naye ku Babiloni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Evili-Merodaki anakomera mtima Yehoyakini, namupatsa malo aulemu kuposa mafumu ena amene anali naye ku Babuloni.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 52:32
6 Mawu Ofanana  

nakamba naye zokoma, namkweza mpando wake waulemu upose mipando ya mafumu anali pamodzi naye mu Babiloni.


Nkhawa iweramitsa mtima wa munthu; koma mau abwino aukondweretsa.


Pakuti atero Ambuye Yehova, Taona ndidzafikitsira Tiro Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni, mfumu ya mafumu, yochokera kumpoto ndi akavalo, ndi magaleta, ndi apakavalo, ndi msonkhano wa anthu ambiri.


Inu mfumu ndinu mfumu ya mafumu, pakuti Mulungu wa Kumwamba anakupatsani ufumu, ndi mphamvu yaikulu, ndi ulemu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa