Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 52:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo pambali pake panali makangaza makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi limodzi; ndipo makangaza onse anali zana limodzi pamade pozungulira pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo pambali pake panali makangaza makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi limodzi; ndipo makangaza onse anali zana limodzi pamade pozungulira pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Makangaza 96 anali pambali, koma onse pamodzi analipo zana limodzi, kuzungulira ukonde wonsewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Mʼmbali mwake munali makangadza 96; makangadza onse pamodzi analipo 100 kuzungulira ukonde onse.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 52:23
2 Mawu Ofanana  

Ndipo panalinso mitu pamwamba pa nsanamira ziwirizo, pafupi pa mimbayo, inali m'mbali mwake mwa ukondewo; ndipo makangazawo anali mazana awiri, akukhala mizere yozinga ndanda mutu winawo.


Ndipo pa mbinyiru wake upange makangaza a lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, pambinyiru pake pozungulira, ndi kuwapakiza ndi miliu yagolide pozungulira;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa