Yeremiya 52:20 - Buku Lopatulika20 Nsanamira ziwirizo, thawale limodzilo, ndi ng'ombe zamkuwa zinali pansi pa zoikapo, zimene mfumu Solomoni anazipangira nyumba ya Yehova; mkuwa wa zipangizo zonsezi sanathe kuyesa kulemera kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Nsanamira ziwirizo, thawale limodzilo, ndi ng'ombe zamkuwa zinali pansi pa zoikapo, zimene mfumu Solomoni anazipangira nyumba ya Yehova; mkuwa wa zipangizo zonsezi sanathe kuyesa kulemera kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Nsanamira ziŵiri zija, chimbiya, maphaka ndiponso ng'ombe zamphongo khumi ndi ziŵiri zimene zinkachirikiza chimbiyacho, zimene mfumu Solomoni adaapangira Nyumba ya Chauta kulemera kwake kwa mkuŵa wa zonsezo kunali kosaŵerengeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Nsanamira ziwiri zija, chimbiya, maphaka ndi ngʼombe khumi ndi ziwiri za mkuwa zochirikizira chimbiyacho zimene mfumu Solomoni anapangira Nyumba ya Yehova kulemera kwake kunali kosawerengeka. Onani mutuwo |