Yeremiya 51:61 - Buku Lopatulika61 Ndipo Yeremiya anati kwa Seraya, Pamene ufika ku Babiloni, samalira kuti uwerenge mau awa onse, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201461 Ndipo Yeremiya anati kwa Seraya, Pamene ufika ku Babiloni, samalira kuti uwerenge mau awa onse, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa61 Yeremiyayo adauza Seraya kuti, “Pamene ukafike ku Babiloni, usakalephere kuŵaŵerengera anthu mau onseŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero61 Yeremiya anawuza Seraya kuti, “Ukakafika ku Babuloni, ukaonetsetse kuti wawawerengera anthu onse mawu onsewa. Onani mutuwo |