Yeremiya 51:23 - Buku Lopatulika23 ndi iwe ndidzathyolathyola mbusa ndi zoweta zake; ndi iwe ndidzathyolathyola wakulima ndi goli la ng'ombe lake; ndi iwe ndidzathyolathyola akazembe ndi ziwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndi iwe ndidzathyolathyola mbusa ndi zoweta zake; ndi iwe ndidzathyolathyola wakulima ndi goli la ng'ombe lake; ndi iwe ndidzathyolathyola akazembe ndi ziwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndi iwe ndimaphwanyaphwanya abusa ndi ziŵeto zao. Ndi iwe ndimaphwanyaphwanya alimi ndi ng'ombe zao. Ndi iwe ndimaphwanyaphwanya abwanamkubwa ndi atsogoleri ankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndi iwe ndimaphwanya mʼbusa ndi ziweto, ndi iwe ndimaphwanya mlimi ndi ngʼombe, ndi iwe ndimaphwanya abwanamkubwa ndi atsogoleri a ankhondo. Onani mutuwo |