Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 5:30 - Buku Lopatulika

30 Chodabwitsa ndi choopsa chaoneka m'dzikomo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Chodabwitsa ndi choopsa chaoneka m'dzikomo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 M'dziko muno mwachitika chinthu chododometsa ndi choopsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 “Chinthu chothetsa nzeru ndi choopsa kwambiri chachitika mʼdzikomo:

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 5:30
5 Mawu Ofanana  

Imvani, miyamba inu, tchera makutu, iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena, Ndakulitsa ndipo ndalera ana, ndipo iwo anandipandukira Ine.


Chifukwa chake atero Yehova; Funsanitu m'mitundu, ndani wamva zotero; namwali wa Israele wachita chinthu choopsetsa kwambiri.


Muzizwe pamenepo, miyamba inu, muope kwambiri, mukhale ouma, ati Yehova.


Mwa aneneri a ku Yerusalemu ndinaona chinthu choopsetsa; achita chigololo, ayenda monama, alimbitsa manja a ochita zoipa, ndipo palibe wobwerera kuleka zoipa zake; onse akhala kwa Ine ngati Sodomu, ndi okhalamo ake ngati Gomora.


M'nyumba ya Israele ndinaona chinthu choopsetsa; pamenepo pali uhule wa Efuremu; Israele wadetsedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa