Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 5:20 - Buku Lopatulika

20 Nenani ichi m'nyumba ya Yakobo, lalikirani mu Yuda, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Nenani ichi m'nyumba ya Yakobo, lalikirani m'Yuda, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Mulalike kwa ana a Yakobe, mulengeze kwa anthu a ku Yuda kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 “Lengeza izi kwa ana a Yakobo ndipo mulalikire kwa anthu a ku Yuda kuti,

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 5:20
3 Mawu Ofanana  

Nenani mu Yuda, lalikirani mu Yerusalemu, ndi kuti, Ombani lipenga m'dzikomo; fuulani, ndi kuti, Sonkhanani pamodzi, tilowe m'mizinda ya malinga.


Ndipo padzakhala pamene mudzati, Chifukwa chanji Yehova Mulungu wathu atichitira ife zonse izi? Ndipo udzayankha kwa iwo, Monga ngati mwandisiya Ine, ndi kutumikira milungu yachilendo m'dziko lanu, momwemo mudzatumikira alendo m'dziko silili lanu.


Tamvanitu ichi, inu anthu opusa, ndi opanda nzeru; ali ndi maso koma osaona, ali ndi makutu koma osamva;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa