Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 49:9 - Buku Lopatulika

9 Akafika kwa inu akutchera mphesa, sadzasiya mphesa zokunkha? Akafika usiku akuba, adzaononga mpaka kutha?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Akafika kwa inu akutchera mphesa, sadzasiya mphesa zokunkha? Akafika usiku akuba, adzaononga mpaka kutha?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Othyola mphesa akadakwera kwa inu, akadakusiyiraniko mphesa pa nthambi. Mbala zikadafika usiku, bwenzi zitangotengako zofunikira zokha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kodi anthu othyola mphesa akanafika kwa inu akanakusiyiraniko mphesa pangʼono pokha? Anthu akuba akanafika usiku akanangotengako zimene akuzifuna zokha?

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 49:9
4 Mawu Ofanana  

Koma mudzasiyidwa m'menemo khunkha, monga ngati kugwedeza kwake kwa mtengo wa azitona, zipatso ziwiri pena zitatu m'nsonga ya nthambi yosomphoka, zinai pena zisanu m'nthambi za kunthemba, za mtengo wobalitsa, ati Yehova, Mulungu wa Israele.


Yehova wa makamu atero, Adzakunkha otsalira a Israele monga mpesa; bweza dzanja lako monga wakutchera mphesa m'madengu ake.


Pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa