Yeremiya 48:43 - Buku Lopatulika43 Mantha, ndi dzenje, ndi khwekhwe, zili pa iwe, wokhala mu Mowabu, ati Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Mantha, ndi dzenje, ndi khwekhwe, zili pa iwe, wokhala m'Mowabu, ati Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Nkhaŵa, dzenje ndi msampha zikuyembekeza inu anthu okhala ku Mowabu,” akutero Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Zoopsa, dzenje ndi msampha zikudikira inu anthu a ku Mowabu,” akutero Yehova. Onani mutuwo |