Yeremiya 48:36 - Buku Lopatulika36 Chifukwa chake mtima wanga umlirira Mowabu monga zitoliro, ndipo mtima wanga uwalirira anthu a Kiriheresi monga zitoliro, chifukwa chake zakuchuluka zake adadzionera zatayika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Chifukwa chake mtima wanga umlirira Mowabu monga zitoliro, ndipo mtima wanga uwalirira anthu a Kiriheresi monga zitoliro, chifukwa chake zakuchuluka zake adadzionera zatayika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 “Nchifukwa chake mtima wanga ukulira Mowabu ngati chitoliro. Mtima wanga ukulira anthu a ku Kiriheresi ngati chitoliro, chifukwa chuma chao chonse chimene adaachipata chatheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 “Nʼchifukwa chake mtima wanga ukulirira Mowabu ngati chitoliro. Mtima wanga ukulirira anthu a ku Kiri Heresi ngati chitoliro chifukwa chuma chimene anachipata chatha. Onani mutuwo |