Yeremiya 48:34 - Buku Lopatulika34 Kuyambira kufuula kwa Hesiboni mpaka ku Eleyale, mpaka ku Yahazi anakweza mau, kuyambira pa Zowari mpaka ku Horonaimu, ku Egilati-Selisiya; pakuti pamadzi a ku Nimurimu komwe padzakhala mabwinja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Kuyambira kufuula kwa Hesiboni mpaka ku Eleyale, mpaka ku Yahazi anakweza mau, kuyambira pa Zowari mpaka ku Horonaimu, ku Egilati-Selisiya; pakuti pa madzi a ku Nimurimu komwe padzakhala mabwinja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 “A ku Hesiboni ndi a ku Eleale akulira movutika. Kulira kwao kukumveka mpaka ku Yaza, kuchokera ku Zowari mpaka ku Horonaimu ndi ku Egilati-Selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu aphwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 “A ku Hesiboni ndi Eleali akulira ndipo mfuwu wawo ukumveka mpaka ku Yahazi, kuchokera ku Zowari mpaka ku Horonaimu ndi ku Egilati Selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu aphwa. Onani mutuwo |