Yeremiya 48:31 - Buku Lopatulika31 Chifukwa chake ndidzakuwira Mowabu; inde, ndidzafuulira Mowabu yense, adzalirira anthu a ku Kiriheresi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Chifukwa chake ndidzakuwira Mowabu; inde, ndidzafuulira Mowabu yense, adzalirira anthu a ku Kiriheresi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Motero ndikulira chifukwa cha Mowabu. Ndikulira mwachisoni chifukwa cha anthu onse a ku Mowabu. Ndikulira anthu a ku Kiriheresi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Nʼchifukwa chake ndidzamulira Mowabu, ine ndikulira chifukwa cha anthu onse a ku Mowabu, ndikubuwula chifukwa cha anthu a ku Kiri Heresi. Onani mutuwo |