Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 48:30 - Buku Lopatulika

30 Ine ndidziwa mkwiyo wake, ati Yehova, kuti uli chabe; zonyenga zake sizinachite kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ine ndidziwa mkwiyo wake, ati Yehova, kuti uli chabe; zonyenga zake sizinachita kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Ndikudziŵa kudzikuza kwake. Mau ake odzitama ngachabechabe, ntchito zake nzopanda pake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Ine ndikuzidziwa ntchito zake, akutero Yehova. Ntchitozo ndi nʼzosapindulitsa kanthu.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 48:30
7 Mawu Ofanana  

Yehova aphwanya upo wa amitundu, asandutsa chabe zolingirira za mitundu ya anthu.


Pakuti kukuzaku sikuchokera kum'mawa, kapena kumadzulo, kapena kuchipululu.


Kulibe nzeru ngakhale luntha ngakhale uphungu wotsutsana ndi Yehova.


Ife tinamva kunyada kwa Mowabu, kuti iye ali wonyada ndithu; ngakhale kudzitama kwake, ndi kunyada kwake ndi mkwiyo wake; matukutuku ake ali achabe.


Lupanga lili pa amatukutuku, ndipo adzapusa; lupanga lili pa anthu olimba ake, ndipo adzaopa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa