Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 48:25 - Buku Lopatulika

25 Nyanga ya Mowabu yaduka, ndipo wathyoka mkono wake, ati Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Nyanga ya Mowabu yaduka, ndipo wathyoka mkono wake, ati Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Mphamvu za Mowabu zaonongeka, mkono wake wolimba wathyoka,” akutero Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Mphamvu za Mowabu zawonongeka; mkono wake wathyoka,” akutero Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 48:25
12 Mawu Ofanana  

Unabweza akazi amasiye osawaninkha kanthu, ndi manja a ana amasiye anathyoledwa.


Thyolani mkono wa woipa; ndipo wochimwa, mutsate choipa chake kufikira simuchipezanso china.


Pakuti manja a oipa adzathyoledwa, koma Yehova achirikiza olungama.


Ndipo ndidzatseteka nyanga zonse za oipa; koma nyanga za wolungama zidzakwezeka.


Pokwiya moopsa walikha nyanga zonse za Israele; wabweza m'mbuyo dzanja lake lamanja pamaso pa adaniwo, natentha Yakobo ngati moto wamalawi wonyambita mozungulira.


Ndinali kulingilirira za nyangazi, taonani, pakati pa izo panaphuka nyanga ina, ndiyo yaing'ono; patsogolo pake zitatu za nyanga zoyambazi zinazulidwa ndi mizu yomwe; ndipo taonani, m'nyanga m'menemo munali maso ngati maso a munthu, ndi pakamwa palikunena zazikulu.


Ndi tonde wamanyenje ndiye mfumu ya Agriki, ndi nyanga yaikulu ili pakati pamaso ake ndiyo mfumu yoyamba.


Ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, ndipo taonani, munthu ndi chingwe choyesera m'dzanja lake.


Ndipo ana a Rubeni anamanga Hesiboni, ndi Eleyale, ndi Kiriyataimu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa