Yeremiya 48:21 - Buku Lopatulika21 Chiweruzo chafika padziko lachidikha; pa Holoni, ndi pa Yahazi, ndi pa Mefaati; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Chiweruzo chafika pa dziko lachidikha; pa Holoni, ndi pa Yahazi, ndi pa Mefaati; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 “Chiweruzo chafika ku dziko lakumapiri, ndiye kuti mizinda iyi: Holoni, Yaza, Mefati Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Chiweruzo chabwera ku mizinda ya ku mapiri, ndiyo Holoni, Yaza, Mefaati, Onani mutuwo |
Chifukwa chake, pali moyo wanga, ati Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele, Zedi Mowabu adzakhala ngati Sodomu, ndi ana a Amoni ngati Gomora, pochuluka khwisa ndi maenje a mchere, ndi bwinja losatha; otsala a anthu anga adzalanda zao, ndi otsala a mtundu wa anthu anga adzawalandira akhale cholowa chao.