Yeremiya 48:19 - Buku Lopatulika19 Iwe wokhala mu Aroere, ima panjira, nusuzumire umfunse iye amene athawa, ndi mkazi amene apulumuka; nuti, Chachitidwa chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Iwe wokhala m'Aroere, ima panjira, nusuzumire umfunse iye amene athawa, ndi mkazi amene apulumuka; nuti, Chachitidwa chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Inu amene mumakhala ku Aroere, imani m'mbali mwa mseu muziwonerera. Mufunse mwamuna amene wathaŵa ndiponso mkazi amene wapulumuka, munene kuti, ‘Kodi kwagwanji?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Inu amene mumakhala ku Aroeri, imani mʼmbali mwa msewu ndi kumaonerera. Funsani mwamuna amene akuthawa ndiponso mkazi amene wapulumuka, afunseni kuti, ‘Kodi chachitika nʼchiyani?’ ” Onani mutuwo |