Yeremiya 48:17 - Buku Lopatulika17 Inu nonse akumzungulira, mumchitire iye chisoni, inu nonse akudziwa dzina lake; muti, Chibonga cholimba chathyokatu, ndodo yokoma! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Inu nonse akumzungulira, mumchitire iye chisoni, inu nonse akudziwa dzina lake; muti, Chibonga cholimba chathyokatu, ndodo yokoma! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mumvereni chisoni kwambiri inu nonse anansi ake, anzake nonse amene mumamdziŵa. Ndipo munene kuti, ‘Ogo, taonani m'mene yathyokera ndodo yachifumu yamphamvu ija! Taonani m'mene yathyokera ndodo yaulemu ija!’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mulireni kwambiri, inu nonse amene mwamuzungulira, inu nonse amene mumadziwa za kutchuka kwake; nenani kuti, “Taonani momwe yathyokera ndodo yamphamvu yaufumu ija, taonani momwe ndodo yaulemu yathyokera!” Onani mutuwo |