Yeremiya 42:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anaitana Yohanani mwana wake wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, ndi anthu onse kuyambira wamng'ono kufikira wamkulu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anaitana Yohanani mwana wake wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, ndi anthu onse kuyambira wamng'ono kufikira wamkulu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Yeremiya adaitana Yohanani mwana wa Kareya, pamodzi ndi atsogoleri onse a ankhondo amene anali nawo, ndiponso anthu onse, ang'onoang'ono ndi akuluakulu omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho Yeremiya anayitana Yohanani mwana wa Kareya pamodzi ndi atsogoleri onse a ankhondo amene anali naye ndiponso anthu onse, ana ndi akulu omwe. Onani mutuwo |