Yeremiya 42:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ndidzakuchitirani inu chifundo, kuti iye akuchitireni inu chifundo, nakubwezereni inu kudziko lanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ndidzakuchitirani inu chifundo, kuti iye akuchitireni inu chifundo, nakubwezereni inu kudziko lanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndidzakuchitirani chifundo, kotero kuti iyenso adzakuchitirani chifundo ndi kukulolani kuti mukhale m'dziko lanu lino.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndidzakuchitirani chifundo, ndipo mfumuyonso idzakuchitirani chifundo ndi kukulolani kuti mukhale mʼdziko mwanumwanu. Onani mutuwo |