Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 41:17 - Buku Lopatulika

17 ndipo anachoka, natsotsa mu Geruti-Kimuhamu, amene ali ku Betelehemu, kunka kulowa mu Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 ndipo anachoka, natsotsa m'Geruti-Kimuhamu, amene ali ku Betelehemu, kunka kulowa m'Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Adanyamuka ulendo wao nakaima ku Geruti-Kimuhamu, pafupi ndi Betelehemu. Ankafuna kupita ku Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ndipo ananyamuka nayima ku Geruti Kimuhamu pafupi ndi Betelehemu pa ulendo wawo wopita ku Igupto

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 41:17
6 Mawu Ofanana  

ndi kuti, Iai; tidzanka ku Ejipito, kumene sitidzaona nkhondo, sitidzamva kulira kwa lipenga, sitidzamva njala yokhumba mkate; pamenepo tidzakhala;


Yehova wanena za inu, otsala inu a Yuda, Musalowe mu Ejipito; mudziwetu kuti ndakulangizani inu lero.


Koma Yohanani mwana wake wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo, anatenga otsala onse a Yuda, amene anabwera kumitundu yonse kumene anaingitsidwirako kuti akhale m'dziko la Yuda;


ndipo anadza nalowa m'dziko la Ejipito; pakuti sanamvere mau a Yehova; ndipo anadza mpaka ku Tapanesi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa