Yeremiya 41:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anthu onse amene Ismaele anatenga ndende kuwachotsa mu Mizipa anatembenuka nabwera, nanka kwa Yohanani mwana wake wa Kareya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anthu onse amene Ismaele anatenga ndende kuwachotsa m'Mizipa anatembenuka nabwera, nanka kwa Yohanani mwana wake wa Kareya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Anthu onse amene Ismaele adaaŵatenga ukapolo kuchoka nawo ku Mizipa, adabwerera napita kwa Yohanani mwana wa Kareya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Anthu onse amene Ismaeli anawagwira ukapolo ku Mizipa anabwerera ndi kupita kwa Yohanani mwana wa Kareya. Onani mutuwo |