Yeremiya 41:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo panali pamene anthu onse amene anali ndi Ismaele anaona Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, anasekera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo panali pamene anthu onse amene anali ndi Ismaele anaona Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, anasekera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndipo anthu onse amene Ismaele adaaŵagwira ataona Yohanani mwana wa Kareya ndi atsogoleri a magulu ankhondo aja, adasangalala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamene anthu onse amene Ismaeli anawagwira anaona Yohanani mwana wa Kareya pamodzi ndi atsogoleri a ankhondo amene anali naye, anasangalala. Onani mutuwo |