Yeremiya 41:12 - Buku Lopatulika12 anatenga anthu onse, nanka kukamenyena ndi Ismaele mwana wa Netaniya, nampeza pamadzi ambiri a mu Gibiyoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 anatenga anthu onse, nanka kukamenyena ndi Ismaele mwana wa Netaniya, nampeza pa madzi ambiri a m'Gibiyoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 adasonkhanitsa anthu onse amene anali nawo, napita kukamenyana naye nkhondo. Adakampeza ku chidziŵe cha ku Gibiyoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 anatenga ankhondo awo onse kupita kukamenyana ndi Ismaeli mwana wa Netaniya. Anakamupeza kufupi ndi chidziwe chachikulu cha ku Gibiyoni. Onani mutuwo |